Genesis 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno Yehova anaonekera kwa Abulamu n’kumuuza kuti: “Ndidzapereka dziko ili+ kwa mbewu yako.”+ Pambuyo pake, iye anamanga pamalopo guwa lansembe la Yehova, yemwe anaonekera kwa iye. Genesis 17:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Dziko limene ukukhalamo ngati mlendoli,+ ndidzalipereka kwa iwe ndi mbewu yako yobwera pambuyo pako. Dziko lonse la Kanani lidzakhala lawo mpaka kalekale, ndipo ine ndidzakhala Mulungu wawo.”+ Genesis 35:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Dziko limene ndinalipereka kwa Abulahamu ndi Isaki, ndidzalipereka kwa iwe ndi kwa mbewu yako+ yobwera pambuyo pako.”+
7 Ndiyeno Yehova anaonekera kwa Abulamu n’kumuuza kuti: “Ndidzapereka dziko ili+ kwa mbewu yako.”+ Pambuyo pake, iye anamanga pamalopo guwa lansembe la Yehova, yemwe anaonekera kwa iye.
8 Dziko limene ukukhalamo ngati mlendoli,+ ndidzalipereka kwa iwe ndi mbewu yako yobwera pambuyo pako. Dziko lonse la Kanani lidzakhala lawo mpaka kalekale, ndipo ine ndidzakhala Mulungu wawo.”+
12 Dziko limene ndinalipereka kwa Abulahamu ndi Isaki, ndidzalipereka kwa iwe ndi kwa mbewu yako+ yobwera pambuyo pako.”+