Genesis 12:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno, Yehova anagwetsera Farao ndi banja lake miliri yoopsa+ chifukwa cha Sarai, mkazi wa Abulamu.+ Genesis 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pambuyo pake Mulungu anafikira Abimeleki usiku m’maloto n’kumuuza kuti: “Ufatu iwe chifukwa cha mkazi amene watengayu,+ pakuti ndi mkazi wa mwini.”+
17 Ndiyeno, Yehova anagwetsera Farao ndi banja lake miliri yoopsa+ chifukwa cha Sarai, mkazi wa Abulamu.+
3 Pambuyo pake Mulungu anafikira Abimeleki usiku m’maloto n’kumuuza kuti: “Ufatu iwe chifukwa cha mkazi amene watengayu,+ pakuti ndi mkazi wa mwini.”+