Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mbiri 29:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 golide wopangira zinthu zagolide, siliva wopangira zinthu zasiliva, ndi siliva woti amisiri adzagwirire ntchito zonse. Ndani lero ali wokonzeka kupereka mphatso kwa Yehova?”+

  • Yesaya 18:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Pa nthawi imeneyo, Yehova wa makamu+ adzapatsidwa mphatso ndi mtundu wa anthu ataliatali osalala, anthu oopedwa+ ndi mitundu yonse ya anthu. Umenewu ndi mtundu wa anthu amphamvu kwambiri, ndiponso wopambana pa nkhondo, umene nthaka yake yakokoloka ndi mitsinje. Mphatsoyo adzaiika kuphiri la Ziyoni, kumene kuli dzina la Yehova wa makamu.”+

  • Mateyu 5:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 “Choncho ngati wabweretsa mphatso yako paguwa lansembe,+ ndipo uli pomwepo wakumbukira kuti m’bale wako ali nawe chifukwa,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena