Salimo 97:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 97 Yehova wakhala mfumu!+ Dziko lapansi likondwere,+Ndipo zilumba zambiri zisangalale.+ Salimo 98:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Fuulirani Yehova mosangalala chifukwa wapambana, inu nonse anthu a padziko lapansi.+Kondwerani, fuulani mosangalala ndi kuimba nyimbo zomutamanda.+
4 Fuulirani Yehova mosangalala chifukwa wapambana, inu nonse anthu a padziko lapansi.+Kondwerani, fuulani mosangalala ndi kuimba nyimbo zomutamanda.+