7 Pa nthawi yonse imene ndinali kuyendayenda pakati pa ana a Isiraeli onse,+ kodi ndinalankhulapo mawu ndi limodzi mwa mafuko onse a Isiraeli,+ fuko limene ndinalilamula kutsogolera anthu anga Aisiraeli, kuti, ‘N’chifukwa chiyani anthu inu simunandimangire nyumba ya mitengo ya mkungudza?’”’