2 Samueli 7:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pakuti inu Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, mwaululira ine mtumiki wanu kuti, ‘Ndidzakumangira nyumba.’*+ N’chifukwa chake ine mtumiki wanu ndalimba mtima kupemphera kwa inu pemphero lino.+
27 Pakuti inu Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, mwaululira ine mtumiki wanu kuti, ‘Ndidzakumangira nyumba.’*+ N’chifukwa chake ine mtumiki wanu ndalimba mtima kupemphera kwa inu pemphero lino.+