2 Samueli 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Davide anapha Hadadezeri,+ mwana wa Rehobu mfumu ya Zoba,+ pamene Hadadezeriyo anali kupita kumtsinje wa Firate+ kukabwezeretsa ulamuliro wake kumeneko. 1 Mafumu 11:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mulungu anasankha munthu winanso woti azilimbana+ ndi Solomo. Munthuyo anali Rezoni mwana wa Eliyada, yemwe anathawa kwa mbuye wake Hadadezeri,+ mfumu ya Zoba.+
3 Davide anapha Hadadezeri,+ mwana wa Rehobu mfumu ya Zoba,+ pamene Hadadezeriyo anali kupita kumtsinje wa Firate+ kukabwezeretsa ulamuliro wake kumeneko.
23 Mulungu anasankha munthu winanso woti azilimbana+ ndi Solomo. Munthuyo anali Rezoni mwana wa Eliyada, yemwe anathawa kwa mbuye wake Hadadezeri,+ mfumu ya Zoba.+