1 Mafumu 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mfumu Solomo inapanga zishango 200 zikuluzikulu za golide wosakaniza ndi zitsulo zina.+ (Chishango chachikulu chilichonse anachikuta ndi golide wolemera masekeli* 600.)+
16 Mfumu Solomo inapanga zishango 200 zikuluzikulu za golide wosakaniza ndi zitsulo zina.+ (Chishango chachikulu chilichonse anachikuta ndi golide wolemera masekeli* 600.)+