2 Samueli 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mafumu onse+ amene anali atumiki a Hadadezeri, ataona kuti agonja pamaso pa Isiraeli,+ nthawi yomweyo anakhazikitsa mtendere ndi Aisiraeli ndi kuyamba kuwatumikira.+ Asiriya sanayesenso kupulumutsa ana a Amoni chifukwa anali kuchita mantha.+
19 Mafumu onse+ amene anali atumiki a Hadadezeri, ataona kuti agonja pamaso pa Isiraeli,+ nthawi yomweyo anakhazikitsa mtendere ndi Aisiraeli ndi kuyamba kuwatumikira.+ Asiriya sanayesenso kupulumutsa ana a Amoni chifukwa anali kuchita mantha.+