2 Samueli 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Zinthu zimenezi Mfumu Davide inazipatulira Yehova pamodzi ndi siliva ndi golide wochokera ku mitundu yonse imene inagonjetsa.+ 1 Mbiri 18:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Zinthu zimenezi Mfumu Davide inazipatulira+ Yehova pamodzi ndi siliva ndi golide amene inalanda ku mitundu yonse,+ kuchokera ku Edomu, ku Mowabu,+ kwa ana a Amoni,+ Afilisiti,+ ndi Aamaleki.+
11 Zinthu zimenezi Mfumu Davide inazipatulira Yehova pamodzi ndi siliva ndi golide wochokera ku mitundu yonse imene inagonjetsa.+
11 Zinthu zimenezi Mfumu Davide inazipatulira+ Yehova pamodzi ndi siliva ndi golide amene inalanda ku mitundu yonse,+ kuchokera ku Edomu, ku Mowabu,+ kwa ana a Amoni,+ Afilisiti,+ ndi Aamaleki.+