Genesis 32:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kenako munthuyo anati: “Dzina lako silikhalanso Yakobo, koma Isiraeli,*+ pakuti walimbana+ ndi Mulungu ndi anthu, ndipo potsirizira pake wapambana.” Genesis 49:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Bwerani pamodzi nonse kuti mumvetsere, inu ana a Yakobo. Bwerani mumvetsere kwa Isiraeli bambo anu.+
28 Kenako munthuyo anati: “Dzina lako silikhalanso Yakobo, koma Isiraeli,*+ pakuti walimbana+ ndi Mulungu ndi anthu, ndipo potsirizira pake wapambana.”
2 Bwerani pamodzi nonse kuti mumvetsere, inu ana a Yakobo. Bwerani mumvetsere kwa Isiraeli bambo anu.+