Genesis 29:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Anakhalanso ndi pakati pena n’kubereka mwana wamwamuna, ndipo anati: “Tsopano nditamanda Yehova.” Choncho Leya anatcha mwanayo, Yuda.*+ Atabereka mwana ameneyu, anayamba waleka kubereka. Genesis 49:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Koma iwe Yuda,+ abale ako adzakutamanda.+ Dzanja lako lidzakhala pambuyo pa khosi la adani ako.+ Ana a bambo ako adzakugwadira.+ Aheberi 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tonse tikudziwa kuti Ambuye wathu anatuluka m’fuko la Yuda,+ ndipo ponena za fuko limeneli Mose sanatchulepo chilichonse chokhudza ansembe.
35 Anakhalanso ndi pakati pena n’kubereka mwana wamwamuna, ndipo anati: “Tsopano nditamanda Yehova.” Choncho Leya anatcha mwanayo, Yuda.*+ Atabereka mwana ameneyu, anayamba waleka kubereka.
8 “Koma iwe Yuda,+ abale ako adzakutamanda.+ Dzanja lako lidzakhala pambuyo pa khosi la adani ako.+ Ana a bambo ako adzakugwadira.+
14 Tonse tikudziwa kuti Ambuye wathu anatuluka m’fuko la Yuda,+ ndipo ponena za fuko limeneli Mose sanatchulepo chilichonse chokhudza ansembe.