Genesis 23:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mundipemphere kuti andigulitse phanga lake la Makipela+ limene lili m’malire a malo ake. Andigulitse pa mtengo wake wonse inu mukuona, kuti ndiikemo malemu mkazi wanga.”+
9 Mundipemphere kuti andigulitse phanga lake la Makipela+ limene lili m’malire a malo ake. Andigulitse pa mtengo wake wonse inu mukuona, kuti ndiikemo malemu mkazi wanga.”+