2 Samueli 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsiku limenelo, Davide anachita mantha kwambiri chifukwa cha Yehova,+ ndipo anati: “Kodi likasa la Yehova lidzabwera bwanji kumene ine ndikukhala?”+ Salimo 119:120 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 120 Chifukwa choopa inu, thupi langa linagwidwa nthumanzi,+Ndipo chifukwa cha zigamulo zanu, ndinachita mantha.+
9 Tsiku limenelo, Davide anachita mantha kwambiri chifukwa cha Yehova,+ ndipo anati: “Kodi likasa la Yehova lidzabwera bwanji kumene ine ndikukhala?”+
120 Chifukwa choopa inu, thupi langa linagwidwa nthumanzi,+Ndipo chifukwa cha zigamulo zanu, ndinachita mantha.+