Yesaya 64:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Nyumba yathu yoyera ndiponso yokongola+ imene makolo athu anali kukutamandiranimo,+ yasanduka chinthu chofunika kuchitentha pamoto,+ ndipo zinthu zathu zonse zabwinozabwino+ zasakazidwa. Hagai 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 ‘Kodi pakati panu pali wotsala aliyense amene anaona ulemerero umene nyumbayi inali nawo poyamba?+ Kodi panopa mukuiona bwanji? Kodi simukuona kuti ilibe ulemerero poyerekeza ndi ulemerero umene inali nawo poyamba?’+
11 Nyumba yathu yoyera ndiponso yokongola+ imene makolo athu anali kukutamandiranimo,+ yasanduka chinthu chofunika kuchitentha pamoto,+ ndipo zinthu zathu zonse zabwinozabwino+ zasakazidwa.
3 ‘Kodi pakati panu pali wotsala aliyense amene anaona ulemerero umene nyumbayi inali nawo poyamba?+ Kodi panopa mukuiona bwanji? Kodi simukuona kuti ilibe ulemerero poyerekeza ndi ulemerero umene inali nawo poyamba?’+