Genesis 30:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Zitatero, Rakele anati: “Mulungu wakhala monga woweruza+ wanga ndipo wamvera mawu anga, choncho wandipatsa mwana wamwamuna.” N’chifukwa chake Rakele anatcha mwanayo dzina lakuti Dani.*+ Genesis 49:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Dani adzaweruza anthu a mtundu wake monga mmodzi wa mafuko a Isiraeli.+
6 Zitatero, Rakele anati: “Mulungu wakhala monga woweruza+ wanga ndipo wamvera mawu anga, choncho wandipatsa mwana wamwamuna.” N’chifukwa chake Rakele anatcha mwanayo dzina lakuti Dani.*+