2 Samueli 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 inauza Natani+ mneneri kuti: “Tsopano taona, ine ndikukhala m’nyumba ya mitengo ya mkungudza,+ pamene likasa la Mulungu woona likukhala m’chihema chansalu.”+ 1 Mafumu 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndipo bambo anga Davide, anafuna mumtima mwawo kumanga nyumba ya dzina la Yehova Mulungu wa Isiraeli.+ Salimo 132:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kufikira Yehova nditamupezera nyumba,+Kufikira nditapeza chihema chachikulu cha Wamphamvu wa Yakobo.”+
2 inauza Natani+ mneneri kuti: “Tsopano taona, ine ndikukhala m’nyumba ya mitengo ya mkungudza,+ pamene likasa la Mulungu woona likukhala m’chihema chansalu.”+
17 Ndipo bambo anga Davide, anafuna mumtima mwawo kumanga nyumba ya dzina la Yehova Mulungu wa Isiraeli.+
5 Kufikira Yehova nditamupezera nyumba,+Kufikira nditapeza chihema chachikulu cha Wamphamvu wa Yakobo.”+