Genesis 30:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Chotero Rakele anatcha mwanayo dzina lakuti Yosefe,*+ ndipo anati: “Yehova wandiwonjezera mwana wina wamwamuna.” Genesis 49:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Yosefe ndi mphukira yamtengo wobala zipatso.+ Ndithu iye ndi mphukira yamtengo wobala zipatso pakasupe.+ Iye ndi mtengo woponya nthambi zake pamwamba pa khoma* la mpanda.+
24 Chotero Rakele anatcha mwanayo dzina lakuti Yosefe,*+ ndipo anati: “Yehova wandiwonjezera mwana wina wamwamuna.”
22 “Yosefe ndi mphukira yamtengo wobala zipatso.+ Ndithu iye ndi mphukira yamtengo wobala zipatso pakasupe.+ Iye ndi mtengo woponya nthambi zake pamwamba pa khoma* la mpanda.+