1 Mbiri 24:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mwa mbadwa za Izara,+ panali Selomoti.+ Pa ana a Selomoti panali Yahati.