1 Mafumu 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ine ndakwanitsa kukumangirani nyumba yomwe ndi malo anu okhalamo okwezeka,+ malo okhazikika+ oti mukhalemo mpaka kalekale.”+ Salimo 135:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yehova amene akukhala ku Yerusalemu,+Atamandidwe mu Ziyoni.+Tamandani Ya, anthu inu!+
13 Ine ndakwanitsa kukumangirani nyumba yomwe ndi malo anu okhalamo okwezeka,+ malo okhazikika+ oti mukhalemo mpaka kalekale.”+