Genesis 38:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma Ere, mwana woyamba wa Yuda, anakhala munthu woipa pamaso pa Yehova.+ Chotero Yehova anamupha.+
7 Koma Ere, mwana woyamba wa Yuda, anakhala munthu woipa pamaso pa Yehova.+ Chotero Yehova anamupha.+