Luka 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano pamene Zekariya anali kugwira ntchito monga wansembe pamaso pa Mulungu, kuimira gawo lake,+ Luka 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Tsopano masiku ake otumikira atatha,+ anapita kwawo.
8 Tsopano pamene Zekariya anali kugwira ntchito monga wansembe pamaso pa Mulungu, kuimira gawo lake,+