1 Mbiri 27:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ana ena a Perezi+ anali akuluakulu a anthu amene anali kutumikira monga atsogoleri a asilikali. Nawonso ankatumikira mwezi woyamba.
3 Ana ena a Perezi+ anali akuluakulu a anthu amene anali kutumikira monga atsogoleri a asilikali. Nawonso ankatumikira mwezi woyamba.