Yoswa 13:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Gawo lawo linayambira kumzinda wa Yazeri,+ mizinda yonse ya ku Giliyadi,+ ndi hafu ya dziko la ana a Amoni,+ mpaka kukafika ku Aroweli+ kufupi ndi Raba.+ Yoswa 21:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Hesiboni+ ndi malo ake odyetserako ziweto, ndiponso Yazeri+ ndi malo ake odyetserako ziweto. Yonse pamodzi inalipo mizinda inayi.
25 Gawo lawo linayambira kumzinda wa Yazeri,+ mizinda yonse ya ku Giliyadi,+ ndi hafu ya dziko la ana a Amoni,+ mpaka kukafika ku Aroweli+ kufupi ndi Raba.+
39 Hesiboni+ ndi malo ake odyetserako ziweto, ndiponso Yazeri+ ndi malo ake odyetserako ziweto. Yonse pamodzi inalipo mizinda inayi.