Genesis 31:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yakobo anathawa n’kuwoloka Mtsinje*+ limodzi ndi zonse zimene anali nazo. Atatero, anayenda molunjika dera la kumapiri la Giliyadi.+ 1 Samueli 13:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Aheberi ena mpaka anawoloka Yorodano+ kupita m’dera la Gadi+ ndi la Giliyadi. Koma Sauli anali adakali ku Giligala, ndipo anthu onse anali kunjenjemera pamene anali kum’tsatira.+
21 Yakobo anathawa n’kuwoloka Mtsinje*+ limodzi ndi zonse zimene anali nazo. Atatero, anayenda molunjika dera la kumapiri la Giliyadi.+
7 Aheberi ena mpaka anawoloka Yorodano+ kupita m’dera la Gadi+ ndi la Giliyadi. Koma Sauli anali adakali ku Giligala, ndipo anthu onse anali kunjenjemera pamene anali kum’tsatira.+