1 Mafumu 8:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma iweyo sumanga nyumbayi, m’malomwake mwana wako wamwamuna wotuluka m’chiuno mwako ndi amene adzamange nyumba ya dzina langa.’+ 1 Mbiri 28:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndipo pa ana anga onse (pakuti Yehova wandipatsa ana ambiri)+ anasankha mwana wanga Solomo+ kuti akhale pampando wachifumu+ wa ufumu wa Yehova, kuti alamulire Isiraeli.
19 Koma iweyo sumanga nyumbayi, m’malomwake mwana wako wamwamuna wotuluka m’chiuno mwako ndi amene adzamange nyumba ya dzina langa.’+
5 Ndipo pa ana anga onse (pakuti Yehova wandipatsa ana ambiri)+ anasankha mwana wanga Solomo+ kuti akhale pampando wachifumu+ wa ufumu wa Yehova, kuti alamulire Isiraeli.