Genesis 50:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yosefe anakhalabe ndi moyo mpaka kuona ana a Efuraimu a m’badwo wachitatu.+ Anaonanso ana a Makiri+ mwana wa Manase. Onsewo anabadwira pamiyendo pa Yosefe.+ Deuteronomo 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Makiri+ ndinam’patsa Giliyadi.+ 1 Mbiri 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mwana wa Manase+ yemwe mdzakazi wake wachisiriya anam’berekera, anali Asiriyeli. (Mdzakaziyo anabereka Makiri,+ bambo wa Giliyadi.
23 Yosefe anakhalabe ndi moyo mpaka kuona ana a Efuraimu a m’badwo wachitatu.+ Anaonanso ana a Makiri+ mwana wa Manase. Onsewo anabadwira pamiyendo pa Yosefe.+
14 Mwana wa Manase+ yemwe mdzakazi wake wachisiriya anam’berekera, anali Asiriyeli. (Mdzakaziyo anabereka Makiri,+ bambo wa Giliyadi.