Numeri 32:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Yairi mwana wa Manase ananyamuka ulendo wokalanda midzi yawo ing’onoing’ono. Midzi imeneyi anaitcha kuti Havoti-yairi.+
41 Yairi mwana wa Manase ananyamuka ulendo wokalanda midzi yawo ing’onoing’ono. Midzi imeneyi anaitcha kuti Havoti-yairi.+