1 Mbiri 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Davide anali atakalamba+ ndiponso atakhutira ndi masiku a moyo wake. Chotero analonga mwana wake Solomo+ kukhala mfumu ya Isiraeli.
23 Davide anali atakalamba+ ndiponso atakhutira ndi masiku a moyo wake. Chotero analonga mwana wake Solomo+ kukhala mfumu ya Isiraeli.