Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mbiri 22:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Zitatha izi, Davide analamula akalonga onse a Isiraeli kuti athandize mwana wake Solomo. Iye anati:

  • 1 Mbiri 28:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Tsopano ndikukupatsa magulu a ansembe+ ndi a Alevi+ ogwira ntchito zonse za panyumba ya Mulungu woona. Pa ntchito yonseyi, uli ndi amisiri odzipereka+ odziwa ntchito zosiyanasiyana,+ ndi akalonga,+ ndiponso anthu onse. Onsewa ndi okonzeka kuchita monga mwa mawu ako.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena