1 Mbiri 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kalebe mwana wa Hezironi+ anabereka ana kudzera mwa Azuba mkazi wake ndiponso kudzera mwa Yerioti. Ana akewo anali: Yeseri, Sobabu, ndi Aridoni.
18 Kalebe mwana wa Hezironi+ anabereka ana kudzera mwa Azuba mkazi wake ndiponso kudzera mwa Yerioti. Ana akewo anali: Yeseri, Sobabu, ndi Aridoni.