Yoswa 15:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Otiniyeli+ mwana wa Kenazi,+ m’bale wake wa Kalebe, analanda mzindawo. Chotero Kalebe anam’patsa Akisa,+ mwana wake, kuti akhale mkazi wake. Oweruza 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndipo Otiniyeli+ mwana wa Kenazi,+ mng’ono wake wa Kalebe, analanda mzindawo.+ Choncho, Kalebe anam’patsa Akisa mwana wake kuti akhale mkazi wake.+
17 Otiniyeli+ mwana wa Kenazi,+ m’bale wake wa Kalebe, analanda mzindawo. Chotero Kalebe anam’patsa Akisa,+ mwana wake, kuti akhale mkazi wake.
13 Ndipo Otiniyeli+ mwana wa Kenazi,+ mng’ono wake wa Kalebe, analanda mzindawo.+ Choncho, Kalebe anam’patsa Akisa mwana wake kuti akhale mkazi wake.+