Yoswa 15:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ku Sefela+ kunali Esitaoli,+ Zora,+ Asina, Yoswa 19:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Malire a gawo la cholowa chawo anadutsa ku Zora,+ Esitaoli, Iri-semesi, Oweruza 13:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kenako mzimu wa Yehova+ unayamba kugwira ntchito pa iye ku Mahane-dani+ pakati pa Zora+ ndi Esitaoli.+ Oweruza 16:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kenako abale ake ndi anthu onse a m’nyumba ya bambo ake, anapita kumeneko kukatenga mtembo wa Samisoni ndi kubwera nawo kwawo, ndipo anamuika m’manda a bambo ake Manowa,+ pakati pa Zora+ ndi Esitaoli.+ Samisoni anali ataweruza Isiraeli zaka 20.+
25 Kenako mzimu wa Yehova+ unayamba kugwira ntchito pa iye ku Mahane-dani+ pakati pa Zora+ ndi Esitaoli.+
31 Kenako abale ake ndi anthu onse a m’nyumba ya bambo ake, anapita kumeneko kukatenga mtembo wa Samisoni ndi kubwera nawo kwawo, ndipo anamuika m’manda a bambo ake Manowa,+ pakati pa Zora+ ndi Esitaoli.+ Samisoni anali ataweruza Isiraeli zaka 20.+