Genesis 48:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mngelo amene wakhala akundiwombola ku masoka anga onse,+ adalitse anyamatawa.+ Dzina langa ndi mayina a makolo anga, Abulahamu ndi Isaki, apitirize kutchulidwa kudzela mwa anawa,+Komanso, anawa adzachulukane, adzakhale khamu la anthu padziko lapansi.”+ Salimo 50:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pa tsiku la nsautso undiitane.+Ine ndidzakulanditsa, ndipo iwe udzandilemekeza.”+
16 Mngelo amene wakhala akundiwombola ku masoka anga onse,+ adalitse anyamatawa.+ Dzina langa ndi mayina a makolo anga, Abulahamu ndi Isaki, apitirize kutchulidwa kudzela mwa anawa,+Komanso, anawa adzachulukane, adzakhale khamu la anthu padziko lapansi.”+