Salimo 21:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mwaipatsa zokhumba za mtima wake,+Ndipo simunaimane zokhumba za pakamwa pake.+ [Seʹlah.] Salimo 66:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndithudi, Mulungu wamva,+Wamvetsera mwatcheru mawu a pemphero langa.+ Mateyu 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Pemphanibe,+ ndipo adzakupatsani. Pitirizani kufunafuna, ndipo mudzapeza. Gogodanibe,+ ndipo adzakutsegulirani. Mateyu 21:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chinthu chilichonse chimene mudzapempha m’mapemphero anu, mudzalandira ngati muli ndi chikhulupiriro.”+ 1 Petulo 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti maso+ a Yehova* ali pa olungama, ndipo makutu ake amamva pembedzero lawo,+ koma nkhope ya Yehova imakwiyira anthu ochita zoipa.”+ 1 Yohane 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ifetu timamudalira+ kuti chilichonse chimene tingamupemphe mogwirizana ndi chifuniro chake, amatimvera.+
7 “Pemphanibe,+ ndipo adzakupatsani. Pitirizani kufunafuna, ndipo mudzapeza. Gogodanibe,+ ndipo adzakutsegulirani.
22 Chinthu chilichonse chimene mudzapempha m’mapemphero anu, mudzalandira ngati muli ndi chikhulupiriro.”+
12 Pakuti maso+ a Yehova* ali pa olungama, ndipo makutu ake amamva pembedzero lawo,+ koma nkhope ya Yehova imakwiyira anthu ochita zoipa.”+
14 Ifetu timamudalira+ kuti chilichonse chimene tingamupemphe mogwirizana ndi chifuniro chake, amatimvera.+