Numeri 32:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma Kalebe+ mwana wa Yefune Mkenizi, ndi Yoswa+ mwana wa Nuni, adzaiona nthakayo chifukwa akhala akumvera Yehova ndi mtima wonse.’ Yoswa 15:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kalebe+ mwana wa Yefune anam’patsa gawo lake pakati pa ana a Yuda pomvera lamulo la Yehova kwa Yoswa. Anam’patsa Kiriyati-ariba, kutanthauza Heburoni.+ (Ariba anali tate wa Anaki.)
12 Koma Kalebe+ mwana wa Yefune Mkenizi, ndi Yoswa+ mwana wa Nuni, adzaiona nthakayo chifukwa akhala akumvera Yehova ndi mtima wonse.’
13 Kalebe+ mwana wa Yefune anam’patsa gawo lake pakati pa ana a Yuda pomvera lamulo la Yehova kwa Yoswa. Anam’patsa Kiriyati-ariba, kutanthauza Heburoni.+ (Ariba anali tate wa Anaki.)