Numeri 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Wa fuko la Yuda anali Kalebe,+ mwana wa Yefune. Numeri 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo Yoswa mwana wa Nuni,+ ndi Kalebe mwana wa Yefune,+ amene anakazonda nawo dzikolo, anang’amba zovala zawo.+ Yoswa 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsopano ana a Yuda anapita kwa Yoswa ku Giligala.+ Ndipo Kalebe+ mwana wa Yefune Mkenizi,+ anauza Yoswa kuti: “Inu mukudziwa bwino za mawu amene Yehova analankhula+ kwa Mose munthu wa Mulungu woona,+ onena za ine ndi inu ku Kadesi-barinea.+
6 Ndipo Yoswa mwana wa Nuni,+ ndi Kalebe mwana wa Yefune,+ amene anakazonda nawo dzikolo, anang’amba zovala zawo.+
6 Tsopano ana a Yuda anapita kwa Yoswa ku Giligala.+ Ndipo Kalebe+ mwana wa Yefune Mkenizi,+ anauza Yoswa kuti: “Inu mukudziwa bwino za mawu amene Yehova analankhula+ kwa Mose munthu wa Mulungu woona,+ onena za ine ndi inu ku Kadesi-barinea.+