Genesis 49:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Koma iwe Yuda,+ abale ako adzakutamanda.+ Dzanja lako lidzakhala pambuyo pa khosi la adani ako.+ Ana a bambo ako adzakugwadira.+ Numeri 26:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Amenewa ndiwo anali mabanja a Yuda.+ Amuna onse owerengedwa m’mabanja awo analipo 76,500.+
8 “Koma iwe Yuda,+ abale ako adzakutamanda.+ Dzanja lako lidzakhala pambuyo pa khosi la adani ako.+ Ana a bambo ako adzakugwadira.+