-
Genesis 10:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Amenewa ndiwo anali ana a Hamu monga mwa mabanja awo, monga mwa zilankhulo zawo, m’mayiko awo, mwa mitundu yawo.
-