Numeri 32:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Tsopano ana a Gadi anayamba kumanga mizinda ya Diboni,+ Ataroti,+ Aroweli,+ Deuteronomo 2:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Kuchokera ku Aroweli,+ mzinda umene uli m’mbali mwa chigwa cha Arinoni, ndiponso kuchokera kumzinda wa m’chigwa mpaka ku Giliyadi, panalibe mzinda womwe unali wa malinga aatali kwambiri kwa ife.+ Yehova Mulungu wathu anawapereka onsewo kwa ife.
36 Kuchokera ku Aroweli,+ mzinda umene uli m’mbali mwa chigwa cha Arinoni, ndiponso kuchokera kumzinda wa m’chigwa mpaka ku Giliyadi, panalibe mzinda womwe unali wa malinga aatali kwambiri kwa ife.+ Yehova Mulungu wathu anawapereka onsewo kwa ife.