Deuteronomo 4:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Dera limeneli linayambira ku Aroweli+ m’mphepete mwa chigwa* cha Arinoni mpaka kuphiri la Sione, limene ndi phiri la Herimoni,+ Salimo 42:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Inu Mulungu wanga, ine ndataya mtima.+N’chifukwa chake ndakumbukira inu,+Pamene ndili m’dziko la Yorodano ndi m’mapiri a Herimoni,+Pamene ndili m’phiri laling’ono.+ Salimo 133:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Zili ngati mame+ a ku Herimoni,+Amene akutsikira pamapiri a ku Ziyoni.+Pakuti Yehova analamula dalitso kukhala kumeneko,+Walamulanso kuti kukhale moyo mpaka kalekale.+
48 Dera limeneli linayambira ku Aroweli+ m’mphepete mwa chigwa* cha Arinoni mpaka kuphiri la Sione, limene ndi phiri la Herimoni,+
6 Inu Mulungu wanga, ine ndataya mtima.+N’chifukwa chake ndakumbukira inu,+Pamene ndili m’dziko la Yorodano ndi m’mapiri a Herimoni,+Pamene ndili m’phiri laling’ono.+
3 Zili ngati mame+ a ku Herimoni,+Amene akutsikira pamapiri a ku Ziyoni.+Pakuti Yehova analamula dalitso kukhala kumeneko,+Walamulanso kuti kukhale moyo mpaka kalekale.+