1 Mbiri 16:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Anasiya Hemani+ ndi Yedutuni+ limodzi ndi amuna aja kuti aziimba malipenga,+ zinganga ndi zipangizo zina zoimbira nyimbo ya Mulungu woona, ndipo ana+ a Yedutuni anali alonda a pachipata. Salimo 68:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Oimba nyimbo anali patsogolo, oimba zoimbira za zingwe anali pambuyo pawo,+Pakati panali atsikana akuimba maseche.+
42 Anasiya Hemani+ ndi Yedutuni+ limodzi ndi amuna aja kuti aziimba malipenga,+ zinganga ndi zipangizo zina zoimbira nyimbo ya Mulungu woona, ndipo ana+ a Yedutuni anali alonda a pachipata.
25 Oimba nyimbo anali patsogolo, oimba zoimbira za zingwe anali pambuyo pawo,+Pakati panali atsikana akuimba maseche.+