1 Mbiri 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Eleazara+ anabereka Pinihasi,+ Pinihasi anabereka Abisuwa,+ 1 Mbiri 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pinihasi+ mwana wa Eleazara+ ndiye anali mtsogoleri wawo kalekale, ndipo Yehova anali naye.+