2 Samueli 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mkwiyo wa Yehova unayakiranso+ Isiraeli pamene winawake anaukira Isiraeli mwa kulimbikitsa Davide kuti: “Pita ukawerenge+ anthu a Isiraeli ndi Yuda.” 1 Mbiri 21:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Atafika kumeneko, Yowabu anapereka chiwerengero chonse cha anthu kwa Davide. Aisiraeli onse analipo 1,100,000, amuna ogwira lupanga,+ ndipo amuna a Yuda ogwira lupanga analipo 470,000.
24 Mkwiyo wa Yehova unayakiranso+ Isiraeli pamene winawake anaukira Isiraeli mwa kulimbikitsa Davide kuti: “Pita ukawerenge+ anthu a Isiraeli ndi Yuda.”
5 Atafika kumeneko, Yowabu anapereka chiwerengero chonse cha anthu kwa Davide. Aisiraeli onse analipo 1,100,000, amuna ogwira lupanga,+ ndipo amuna a Yuda ogwira lupanga analipo 470,000.