1 Mbiri 12:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 A fuko la Isakara,+ amene anali ndi nzeru zotha kudziwa nthawi,+ ndi zimene Aisiraeli ayenera kuchita,+ analipo atsogoleri 200, ndipo iwo anali kulamulira abale awo onse.
32 A fuko la Isakara,+ amene anali ndi nzeru zotha kudziwa nthawi,+ ndi zimene Aisiraeli ayenera kuchita,+ analipo atsogoleri 200, ndipo iwo anali kulamulira abale awo onse.