Numeri 26:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Ana aamuna a Benjamini+ ndi mabanja awo anali awa: Bela+ amene anali kholo la banja la Abela, Asibeli+ amene anali kholo la banja la Aasibeli, Ahiramu amene anali kholo la banja la Aahiramu, 1 Mbiri 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Benjamini+ anabereka Bela+ mwana wake woyamba, wachiwiri anali Asibeli,+ wachitatu anali Ahara,+
38 Ana aamuna a Benjamini+ ndi mabanja awo anali awa: Bela+ amene anali kholo la banja la Abela, Asibeli+ amene anali kholo la banja la Aasibeli, Ahiramu amene anali kholo la banja la Aahiramu,