Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 26:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Ana aamuna a Giliyadi anali awa: Yezeri+ amene anali kholo la banja la Ayezeri, Heleki amene anali kholo la banja la Aheleki,

  • Oweruza 6:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Kenako, kunabwera mngelo wa Yehova+ ndi kukhala pansi pa mtengo waukulu umene unali ku Ofira. Mtengo umenewu unali wa Yowasi, Mwabi-ezeri.+ Pa nthawiyi, Gidiyoni+ mwana wa Yowasi, anali kupuntha tirigu moponderamo mphesa kuti akamubise mwamsanga Amidiyani asanaone.

  • Oweruza 8:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Chotero iye anawayankha kuti: “Kodi ine ndachita chiyani poyerekeza ndi inu?+ Kodi zokunkha za Efuraimu+ si zabwino kwambiri kuposa mphesa zimene Abi-ezeri+ wakolola?

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena