Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 5:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Chotero anatumiza uthenga ndi kusonkhanitsa olamulira onse ogwirizana a Afilisiti ku Asidodi ndi kuwauza kuti: “Tichite nalo chiyani likasa la Mulungu wa Isiraeli?” Pamapeto pake iwo anati: “Likasa limeneli la Mulungu wa Isiraeli tilitumize kumzinda wa Gati.”+ Choncho anapititsa likasa la Mulungu wa Isiraeli kumeneko atayenda nalo mozungulira.

  • 1 Samueli 7:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Pamenepo, mizinda imene Afilisitiwo analanda Isiraeli inayamba kubwerera kwa Isiraeli, kuyambira ku Ekironi mpaka ku Gati, ndipo Aisiraeli analanda dera la mizindayo m’manja mwa Afilisiti.

      Choncho panakhala mtendere pakati pa Isiraeli ndi Aamori.+

  • 1 Samueli 17:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndiyeno kumsasa wa Afilisiti kunatuluka ngwazi, dzina lake Goliyati,+ wa ku Gati.+ Iye anali wamtali mikono 6 ndi chikhatho chimodzi.*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena