Salimo 128:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mkazi wako adzakhala ngati mtengo wa mpesa wobala zipatso+Mkati mwa nyumba yako.Ana ako adzakhala ngati mphukira za mitengo ya maolivi+ kuzungulira tebulo lako.
3 Mkazi wako adzakhala ngati mtengo wa mpesa wobala zipatso+Mkati mwa nyumba yako.Ana ako adzakhala ngati mphukira za mitengo ya maolivi+ kuzungulira tebulo lako.