Ekisodo 33:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamenepo Yehova anali kulankhula ndi Mose pamasom’pamaso,+ mmene munthu amalankhulira ndi munthu mnzake. Mose akabwerera kumsasa, mtumiki wake+ Yoswa, mwana wa Nuni,+ sanali kuchoka m’chihemacho, popeza anali kalinde. Yoswa 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Mose mtumiki wa Yehova atamwalira, Yehova analankhula ndi Yoswa+ mwana wa Nuni, mtumiki+ wa Mose, kuti:
11 Pamenepo Yehova anali kulankhula ndi Mose pamasom’pamaso,+ mmene munthu amalankhulira ndi munthu mnzake. Mose akabwerera kumsasa, mtumiki wake+ Yoswa, mwana wa Nuni,+ sanali kuchoka m’chihemacho, popeza anali kalinde.
1 Mose mtumiki wa Yehova atamwalira, Yehova analankhula ndi Yoswa+ mwana wa Nuni, mtumiki+ wa Mose, kuti: